Abstracti

 

Dziwani

kuti zomwe takhala tiri kufufuza poganiza kufunika kwache, koti tipeze mu CXR kuti tithandauze kuchokera mumapapu odziwa bwino pantchito yawo, Erythrocyte Sedimentation Rate (ESR), White Blood Cell Count (WBC) ndi Haemoglobin-level (Hb) pamakhala zomwe zinapezeka m’makhololo zosatila zake kuti sanapezeke ndi chifuwa chachikulu.

 

Malo

Zipatala ziwiri za zing’ono zamuchigawo cha ku m’mwera kwa Malawi kwa amene ali ndi HIV odwala TB ndi 80%.

 

Njira

Zomwe za retrospectively constructed cohort a chifuwa cha chikulu , omwe anayezedwa makhololo, atalandi mankhwala koma, mankhwalawo samathandize ai, atasatila pakutha mwezi 11.

 

Yankho lomwe

Linapeze ka kwa anthu pagulu opanda chititezo cha mthupi lawo omwe sali ndi chifuwa chachikulu mu CXR osika WBC ndi ESR wa 100-124 mm/hr chikana ochepa magazi low Hb pamezi itatu yokha, kunapezeka kuti odwala chifuwa chachikulu. CXR ndi idwala omwe WBC inali yokwera.

 

Posiliza

 zomwe tapeza odwala chifuwa chachikulu chakwera kwambiri chifukwa cha HIV komanso omwe akuoneka kuti alibe chitetezo chamatenda muthupi mwawo uko bvuta tikawayeza odwala makhololo ndi CXR palimbe umboni weni weni woti akudwala chifuwa chachi kulu zosatila zake sizimaoneka bwino ai ochilisa chibayo. Maka maka kwa modwala omwe amapezeka kuti magazi awo a WBC nambala yake ndi yokwela kwambiri high WBC.